Levitiko 22:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92) Ndipo Yehova ananena ndi Mose, ndi kuti, Nena ndi Aroni ndi ana ace amuna, kuti azikhala padera ndi zinthu