Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 22:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nena ndi Aroni ndi ana ace amuna, kuti azikhala padera ndi zinthu zopatulika za ana a Israyeli, zimene amandipatulira Ine, ndipo asaipse dzina langa loyera; Ine ndine Yehova.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 22

Onani Levitiko 22:2 nkhani