Efraimu adzati, Ndiri ndi cianinso ndi mafano? Ndayankha, ndidzampenyerera; ndiri ngati mtengo wamlombwa wabiriwiri; zipatso zako zipezeka zocokera kwa Ine.