Ndipo ukalankhule naye, ndi kumpangira mau; ndipo Ine ndidzakhala m'kamwa mwako, ndi m'kamwa mwace, ndipo ndidzakuphunzitsani inu cimene mukacite.