Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 4:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo mkwiyo wa Yehova unamyakira Mose, ndipo anati, Nanga Aroni Mlevi mbale wako sialipo kodi? Ndidziwa kuti kulankhula alankhula. Ndipo, taona, aturuka kudzakomana ndiwe; ndipo pakuona iwe adzakondweram'mtima mwace.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 4

Onani Eksodo 4:14 nkhani