Kuopa kwakukuru ndi mantha ziwagwera;Pa dzanja lanu lalikuru akhala cete ngati mwala;Kufikira apita anthu anu, Yehova,Kufikira apita anthu amene mudawaombola.