Pamenepo mafumu a Edomu anadabwa;Agwidwa nako kunthunthumira amphamvu a ku Moabu;Okhala m'Kanani onse asungunukamtima.