Nyimbo yolemekeza Mulungu, Pamenepo Mose ndi ana a Israyeli anayimbira Yehova nyimbo iyi, nanena, ndi kuti,Ndidzayimbira Yehova pakuti wapambanatu;Kavalo ndi wokwera wace anawaponya m'nyanja.