Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 15:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Yehova ndiye mphamvu yanga ndi nyimbo yanga,Ndipo wakhala cipulumutso canga;Ameneyo ndiye Mulungu wanga, ndidzamlemekeza:Ndiye Mulungu wa kholo langa, ndidzammveketsa.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 15

Onani Eksodo 15:2 nkhani