Kwera kumwamba ku Pisiga, nukweze maso ako kumadzulo, ndi kumpoto, ndi kumwela, ndi kum'mawa, nuyang'ane ndi maso ako; popeza sudzaoloka Yordano uyo.