koma ndidzatumiza moto pa Moabu, udzanyeketsa nyumba zacifumu za Kerioti; ndipo Moabu adzafa ndi phokoso, ndi kupfuula, ndi mau a lipenga;