Ndipo anaceuka, nawaona, nawatemberera m'dzina la Yehova. Ndipo kuthengo kunaturuka zimbalangondo ziwiri zazikazi, ndi kupwetedza mwa iwo ana makumi anai mphambu awiri.