Ndipo anacokako kukwera ku Beteli, ndipo iye ali cikwerere m'njiramo, munaturuka anyamata ang'ono m'mudzimo, namseka, nati kwa iye, Takwera wadazi, takwera wadazi!