Ninena naye, Ndiye munthu wobvala zaubweya, namangira m'cuuno mwace ndi lamba lacikopa. Nati iye, Ndiye Eliya wa ku Tisibe.