Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 1:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo mfumu inatuma kwa iye asilikari makumi asanu ndi mtsogoleri wao. Iye nakwera kumka kwa Eliya; ndipo taonani, analikukhala pamwamba pa phiri. Ndipo analankhula naye, Munthu wa Mulungu iwe, mfumu ikuti, Tsika.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 1

Onani 2 Mafumu 1:9 nkhani