Ndipo Jonatani mwana wa Sauli ananyamuka, napita kwa Davide kunkhalangoko, namlimbitsa dzanja lace mwa Mulungu.