Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yuda 1:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

kudzacitira onse ciweruziro, ndi kutsutsa osapembedza onse, pa nchito zao zonse zosapembedza, zimene anazicita kosapembedza, ndi pa zolimba zimene ocimwa osapembedza adalankhula pa iye.

Werengani mutu wathunthu Yuda 1

Onani Yuda 1:15 nkhani