Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yohane 6:51 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

8 Mkate wamoyo wotsika Kumwamba Ndine amene. Ngati munthu wina akadyako mkate umene, adzakhala ndi moyo kosatha. Inde, ndipo 9 mkate umene ndidzapatsa Ine, ndiwo thupi langa, ukhale moyo wa dziko lapansi.

Werengani mutu wathunthu Yohane 6

Onani Yohane 6:51 nkhani