Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yohane 6:35 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Yesu anati kwa iwo, Ine ndine mkate wamoyo; iye amene adza kwa Ine sadzamva njala, ndi iye amene akhulupirira Ine sadzamva ludzu nthawi zonse.

Werengani mutu wathunthu Yohane 6

Onani Yohane 6:35 nkhani