Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yohane 3:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma ciweruziro ndi ici, kuti kuunika kunadza ku dziko lapansi, ndipo anthu anakonda mdima koposa kuunika; pakuti nchito zao zinali zoipa.

Werengani mutu wathunthu Yohane 3

Onani Yohane 3:19 nkhani