Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yohane 21:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo wophunzira uja amene Yesu anamkonda ananena kwa Petro, Ndiye Ambuye. Simoni Petro pakumva kuti ndiye Ambuye, anadzibveka maraya a pathupi, pakuti anali wamarisece, nadziponya yekha m'nyanja.

Werengani mutu wathunthu Yohane 21

Onani Yohane 21:7 nkhani