Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yohane 21:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Indetu, indetu, ndinena ndi iwe, pamene unali mnyamata unadzimangira wekha m'cuuno, ndipo unayenda kumene unafuna; koma pamene udzakalamba udzaturutsa manja ako, ndipo adzakumanga wina, nadzakunyamula kumene sufuna.

Werengani mutu wathunthu Yohane 21

Onani Yohane 21:18 nkhani