Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yohane 21:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pamene atafisula Yesu ananena kwa Simoni Petro, Simoni mwana wa Yona, kodi undikonda Ine koposa awa? Ananena ndi iye, Inde, Ambuye; mudziwa kuti ndikukondani Inu. Ananena naye, Dyetsa ana a nkhosa anga.

Werengani mutu wathunthu Yohane 21

Onani Yohane 21:15 nkhani