Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yohane 2:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Ndipo tsiku lacitatu pariali ukwati m'Kana wa m'Galileya; ndipo amace wa Yesu anali komweko.

2. Ndipo Yesu yemwe ndi akuphunzira ace anaitanidwa ku ukwatiwo.

3. Ndipo pakutha vinyo, amace wa Yesu ananena naye, Alibe vinyo,

Werengani mutu wathunthu Yohane 2