Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yohane 19:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pamene ansembe akulu ndi anyamata anamuona iye, anapfuula nanena, Mpacikeni, mpacikeni, Pilato ananena nao, Mtengeni iye inu nimumpaeike; pakuti ine sindipeza cifukwa mwa: iye.

Werengani mutu wathunthu Yohane 19

Onani Yohane 19:6 nkhani