Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yohane 19:35 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo 3 iye amene anaona, wacita umboni, ndi umboni wace uti woona; ndipo iyeyu adziwa kuti anena zoona, kuti inunso mukakhulupire.

Werengani mutu wathunthu Yohane 19

Onani Yohane 19:35 nkhani