Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yohane 18:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma Simoni Petro analikuimirira ndi kuotha moto. Pomwepo anati kwa iye, Suli iwenso wa akuphunzira ace kodi? Iyeyu anakana, nati, Sindine.

Werengani mutu wathunthu Yohane 18

Onani Yohane 18:25 nkhani