Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yohane 16:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mkazi pamene akuti abale ali naco cisoni, cifukwa yafika nthawi yace; koma pamene wabala mwana, sakumbukilanso kusaukako, cifukwa ca cimwemwe kuti wabadwa munthu ku dziko lapansi.

Werengani mutu wathunthu Yohane 16

Onani Yohane 16:21 nkhani