Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yohane 15:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Ine ndine mpesa weniweni, ndipo Atate wanga ndiye wam'munda.

2. Nthambi iri yonse ya mwa Ine yosabala cipatso, aicotsa; ndi iri y'onse yakubala cipatso, aisadza, kuti ikabale cipatso cocuruka.

3. Mwakhala okonzeka tsopano inu cifukwa ca mau amene ndalankhula ndi inu,

Werengani mutu wathunthu Yohane 15