Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yohane 12:35 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo Yesu anati kwa iwo, Katsala kanthawi kakang'ono ndipo kuunika kuli mwa inu. 1 Yendani pokhala muli nako kuunika, kuti mdima sungakupezeni; ndipo woyenda mumdima sadziwa kumene amukako,

Werengani mutu wathunthu Yohane 12

Onani Yohane 12:35 nkhani