Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yohane 12:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo Mariya m'mene adatenga muyeso umodzi wa mafuta onunkhira bwino a nardo a mtengo wace wapatali, anadzoza mapazi a Yesu, napukuta mapazi ace ndi tsitsi lace; ndipo nyumba inadzazidwa ndi mnunkho wace wa mafutawo.

Werengani mutu wathunthu Yohane 12

Onani Yohane 12:3 nkhani