Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yohane 11:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Koma panali munthu wodwala, Lazaro wa ku Betaniya, wa m'mudzi wa Mariya ndi mbale wace Marita.

2. Koma ndiye Mariya uja anadzoza Ambuye ndi mafuta onunkhira bwino, napukuta mapazi ace ndi tsitsi lace, amene mlongo wace Lazaro anadwala.

Werengani mutu wathunthu Yohane 11