Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yohane 1:24-26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

24. Ndipo otumidwawo analia kwa Marisi.

25. Ndipo anamfunsa iye, nati kwa iye, Koma ubatiza bwanji, ngati suli Kristu, kapena Eliya, kapena Mneneriyo?

26. Yohane anawayankha, nati, 2 Ine ndibatiza ndi madzi; pakati pa inu paimirira amene simumdziwa,

Werengani mutu wathunthu Yohane 1