Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yohane 1:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kulibe munthu anaona Mulungu nthawi zonse; Mwana wobadwa yekha wakukhala pa cifuwa ca Atate, Iyeyu anafotokozera.

Werengani mutu wathunthu Yohane 1

Onani Yohane 1:18 nkhani