Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yakobo 5:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace mubvomerezane wina ndi mnzace macimo anu, ndipo mupempherere wina kwa mnzace kuti muciritsidwe. Pemphero la munthu wolungama likhoza kwakukuru m'macitidweace.

Werengani mutu wathunthu Yakobo 5

Onani Yakobo 5:16 nkhani