Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yakobo 2:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ukhulupirira iwe kuti Mulungu ali mmodzi; ucita bwino; ziwanda zikhulupiranso, ndipo zinthunthumira.

Werengani mutu wathunthu Yakobo 2

Onani Yakobo 2:19 nkhani