Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Tito 3:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti kale ifenso tinali opusa, osamvera, onyengeka, akucitira ukapolo zilakolako ndi zokondweretsa za mitundu mitundu, okhala m'dumbo ndi njiru, odanidwa, odana wina ndi mnzace.

Werengani mutu wathunthu Tito 3

Onani Tito 3:3 nkhani