Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Tito 3:14-15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

14. Ndipo anthu athu aphunzirenso asunge nchito zabwino zofunika, kuti asakhale osabala zipstso.

15. Akulankhula iwe onse akukhala pamodzi ndi ine. Lankhula otikondawo m'cikhulupiriro.Cisomo cikhale ndi inu nonse.

Werengani mutu wathunthu Tito 3