Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Mateyu 9:33 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo m'mene cinaturutsidwa ciwandaco, wosalankhulayo analankhula, ndipo makamu a anthu anazizwa, nanena, Kale lonse sicinaoneke comweco mwa Israyeli.

Werengani mutu wathunthu Mateyu 9

Onani Mateyu 9:33 nkhani