Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Mateyu 9:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yesu anati kwa iwo, Nanga anyamata a nyumba ya ukwati angathe kulira kodi nthawi imene mkwati akhala nao? koma adzafika masiku, pamene mkwati adzacotsedwa kwa iwo, ndipo pomwepo adzasala kudya.

Werengani mutu wathunthu Mateyu 9

Onani Mateyu 9:15 nkhani