Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Mateyu 27:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ansembe akuru anatenga ndalamazo, nati, Sikuloledwa kuziika m'cosonkhera ndalama za Mulungu, cifukwa ndizo mtengo wa mwazi.

Werengani mutu wathunthu Mateyu 27

Onani Mateyu 27:6 nkhani