Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Mateyu 26:39 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anamuka patsogolo pang'ono, nagwa nkhope yace pansi, napemphera, nati, Atate, ngati nkutheka, cikho ici cindipitirire Ine; koma si monga ndifuna Ine, koma lou.

Werengani mutu wathunthu Mateyu 26

Onani Mateyu 26:39 nkhani