Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Mateyu 25:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pomwepo uyo amene analandira ndalama zisanu, anapita kugula nazo malonda, napindulapo ndalama zina zisanu.

Werengani mutu wathunthu Mateyu 25

Onani Mateyu 25:16 nkhani