Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Mateyu 25:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pamene iwo analikumuka kukagula, mkwati anafika; ndipo okonzekawo, analowa naye pamodzi muukwati; ndipo anatseka pakhomo.

Werengani mutu wathunthu Mateyu 25

Onani Mateyu 25:10 nkhani