Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Mateyu 23:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Tsoka inu, atsogoleri akhungu, amene munena, Amene ali yense akalumbira kuchula Kacisi, palibe kanthu; koma amene akalumbira kuchula golidi wa Kacisi, wadzimangirira.

Werengani mutu wathunthu Mateyu 23

Onani Mateyu 23:16 nkhani