Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Mateyu 22:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo akapolo ao anaturukira kunjira, nasonkhanitsa onse amene anawapeza, ngakhale oipa, ngakhale abwino; ndipo ukwatiwo unadzala ndi okhala pacakudya.

Werengani mutu wathunthu Mateyu 22

Onani Mateyu 22:10 nkhani