Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Mateyu 18:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

koma yense amene adzakhumudwitsa kamodzi ka tiana iti, takukhulupirira Ine, kumuyenera iye kuti mphero yaikuru ikolowekedwe m'khosi mwace, namizidwe poya pa nyanja.

Werengani mutu wathunthu Mateyu 18

Onani Mateyu 18:6 nkhani