Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Mateyu 16:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pomwepo Yesu anati kwa ophunzira ace, Ngati munthu afuna kudza pambuyo panga, adzikane yekha, natenge mtanda wace, nanditsate Ine.

Werengani mutu wathunthu Mateyu 16

Onani Mateyu 16:24 nkhani