Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Mateyu 12:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Taona mnyamata wanga, amene ndinamsankha,Wokondedwa wanga, amene moyo wanga ukondwera naye;Pa Iye ndidzaika Mzimu wanga,Ndipo Iye adzalalikira ciweruzo kwa akunja.

Werengani mutu wathunthu Mateyu 12

Onani Mateyu 12:18 nkhani