Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Mateyu 10:26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace musaopa iwo; pakuti palibe kanthu kanabvundikiridwa, kamene sikadzaululidwa; kapena kanthu kobisika, kamene sikadzadziwika.

Werengani mutu wathunthu Mateyu 10

Onani Mateyu 10:26 nkhani